Danieli 7:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma oyera a Mulungu Wamkulu+ adzalandira ufumu+ ndipo ufumuwo udzakhala wawo+ mpaka kalekale, inde kwamuyaya.’ Chivumbulutso 3:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Amene wapambana pankhondo+ ndidzamulola kuti akhale ndi ine pampando wanga wachifumu,+ ngati mmene ine ndinakhalira+ ndi Atate wanga pampando wawo wachifumu nditapambana pankhondo.
18 Koma oyera a Mulungu Wamkulu+ adzalandira ufumu+ ndipo ufumuwo udzakhala wawo+ mpaka kalekale, inde kwamuyaya.’
21 Amene wapambana pankhondo+ ndidzamulola kuti akhale ndi ine pampando wanga wachifumu,+ ngati mmene ine ndinakhalira+ ndi Atate wanga pampando wawo wachifumu nditapambana pankhondo.