Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Chivumbulutso 10
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Zimene Zili Mʼbuku la Chivumbulutso

      • Mngelo wamphamvu amene anali ndi mpukutu waungʼono (1-7)

        • “Nthawi yodikira yatha” (6)

        • Chinsinsi chopatulika chidzakwaniritsidwa (7)

      • Yohane anadya mpukutu waungʼono (8-11)

Chivumbulutso 10:1

Mawu a M'munsi

  • *

    Kapena kuti, “anali atakutidwa ndi mtambo.”

  • *

    Mʼchilankhulo choyambirira, “Mapazi ake anali.”

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mt 17:1, 2

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 155

    Nsanja ya Olonda,

    12/15/1988, tsa. 13

    10/15/1988, tsa. 14

Chivumbulutso 10:2

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 156

    Nsanja ya Olonda,

    10/15/1988, tsa. 14

Chivumbulutso 10:3

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 5:5
  • +Eks 19:16; Chv 4:5; 11:19

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 156-157

    Nsanja ya Olonda,

    10/15/1988, tsa. 19

Chivumbulutso 10:4

Mawu a M'munsi

  • *

    Mʼchilankhulo choyambirira, “Utsekere.”

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 10:8

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 157

    Nsanja ya Olonda,

    10/15/1988, tsa. 19

Chivumbulutso 10:5

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 157

Chivumbulutso 10:6

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 90:2; Chv 4:9
  • +Eks 20:11; Ne 9:6; Sl 146:6

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 157

Chivumbulutso 10:7

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 8:6
  • +Chv 11:15
  • +Mko 4:11
  • +Amo 3:7

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 157-158, 171-172

    Nsanja ya Olonda,

    1/15/1990, ptsa. 19-20

    4/1/1989, tsa. 19

    12/15/1988, ptsa. 13-14

Chivumbulutso 10:8

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 10:4
  • +Chv 10:1, 2

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 158-160

Chivumbulutso 10:9

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eze 2:8

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 158-160

Chivumbulutso 10:10

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yer 15:16
  • +Sl 119:103; Eze 3:1-3

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 158-160

    Nsanja ya Olonda,

    12/15/1988, tsa. 13

    10/15/1988, tsa. 14

Chivumbulutso 10:11

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 158-160

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

Chiv. 10:1Mt 17:1, 2
Chiv. 10:3Chv 5:5
Chiv. 10:3Eks 19:16; Chv 4:5; 11:19
Chiv. 10:4Chv 10:8
Chiv. 10:6Sl 90:2; Chv 4:9
Chiv. 10:6Eks 20:11; Ne 9:6; Sl 146:6
Chiv. 10:7Chv 8:6
Chiv. 10:7Chv 11:15
Chiv. 10:7Mko 4:11
Chiv. 10:7Amo 3:7
Chiv. 10:8Chv 10:4
Chiv. 10:8Chv 10:1, 2
Chiv. 10:9Eze 2:8
Chiv. 10:10Yer 15:16
Chiv. 10:10Sl 119:103; Eze 3:1-3
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Chivumbulutso 10:1-11

Chivumbulutso Chimene Yohane Analandira

10 Kenako ndinaona mngelo wina wamphamvu akutsika kuchokera kumwamba ndipo anali atavala mtambo.* Kumutu kwake kunali utawaleza ndipo nkhope yake inali ngati dzuwa.+ Miyendo yake inali* ngati zipilala zamoto. 2 Mʼdzanja lake, anali ndi mpukutu waungʼono wotambasula. Iye anaponda panyanja ndi phazi lake lakumanja koma ndi phazi lake lakumanzere anaponda pamtunda. 3 Kenako anafuula ndi mawu okweza ngati kubangula kwa mkango.+ Atafuula choncho, panamveka mawu a mabingu 7.+

4 Ndiye mabingu 7 aja atalankhula, ndinkafuna kulemba. Koma ndinamva mawu ochokera kumwamba+ akuti: “Usunge mwachinsinsi* zimene mabingu 7 amenewa alankhula ndipo usazilembe.” 5 Mngelo amene ndinamuona ataimirira panyanja ndi pamtunda uja, anakweza dzanja lake lamanja kumwamba. 6 Iye analumbira mʼdzina la Mulungu amene adzakhale ndi moyo mpaka kalekale,+ amene analenga kumwamba ndi zinthu zonse zimene zili kumeneko, dziko lapansi ndi zinthu zonse zimene zili mmenemo komanso nyanja ndi zinthu zonse zimene zili mmenemo.+ Analumbira kuti: “Nthawi yodikira yatha. 7 Masiku oti mngelo wa 7+ alize lipenga akadzatsala pangʼono kukwana,+ chinsinsi chopatulika+ chimene Mulungu analengeza kwa akapolo ake aneneri,+ monga uthenga wabwino, chidzakwaniritsidwa ndithu.”

8 Kenako ndinamva mawu kuchokera kumwamba+ akulankhulanso ndi ine kuti: “Pita, katenge mpukutu wotambasula umene uli mʼdzanja la mngelo amene waima panyanja ndi pamtunda uja.”+ 9 Choncho ndinapita kwa mngeloyo nʼkumuuza kuti andipatse mpukutu waungʼonowo. Iye anandiuza kuti: “Tenga mpukutuwu udye.+ Ukupweteketsa mʼmimba, koma mʼkamwa mwako ukhala wokoma ngati uchi.” 10 Ndinatengadi mpukutu waungʼonowo mʼdzanja la mngeloyo nʼkuudya.+ Mʼkamwa mwanga unkakoma ngati uchi,+ koma nditaudya mʼmimba mwanga munayamba kupweteka. 11 Ndiye ndinauzidwa kuti: “Uyenera kuneneranso zokhudza mitundu ya anthu, mayiko, zilankhulo ndi mafumu ambiri.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena