16 Kachisi wa M’nthawi ya Solomo
(Onani m’Baibulo lenileni kuti mumvetse izi)
1 Malo Oyera Koposa−1Mf 6:16, 20
2 Zipinda za Kudenga−1Mb 28:11
3 Malo Oyera−2Mb 5:9
5 Yakini−1Mf 7:21
6 Boazi−2Mb 3:17
7 Zipinda Zodyeramo−1Mb 28:12
8 Guwa Lansembe Lamkuwa−2Mb 4:1
9 Bwalo la Mkati−1Mf 6:36
10 Thanki Yamkuwa−1Mf 7:23
11 Zotengera Zamawilo−1Mf 7:27
12 Khomo la M’mbali−1Mf 6:8
13 Zipinda za M’mbali−1Mf 6:5, 6, 10