AHEBERI
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
1
2
Tiziganizira mozama kuposa nthawi zonse (1-4)
Zonse zinaikidwa pansi pa mapazi a Yesu (5-9)
Yesu ndiponso abale ake (10-18)
3
4
Kuopsa kosalowa mumpumulo wa Mulungu (1-10)
Anawalimbikitsa kuti alowe mumpumulo wa Mulungu (11-13)
Yesu, mkulu wa ansembe wapamwamba (14-16)
5
6
Yesetsani kuti mukhale aakulu mwauzimu (1-3)
Anthu amene agwa akupachika kachiwiri Mwana wa Mulungu (4-8)
Chiyembekezo chanu chikhale chotsimikizika (9-12)
Malonjezo a Mulungu ndi odalirika (13-20)
7
8
9
10
Nsembe za nyama zinali zosakwanira (1-4)
Nsembe ya Khristu ndi yothandiza mpaka kalekale (5-18)
Njira yatsopano komanso yamoyo (19-25)
Anawachenjeza zokhudza kuchimwa mwadala (26-31)
Tizikhala olimba mtima komanso achikhulupiriro kuti tipirire (32-39)
11
12
Yesu, Wokwaniritsa chikhulupiriro chathu (1-3)
Osapeputsa chilango cha Yehova (4-11)
Muziwongola njira zimene mapazi anu akuyendamo (12-17)
Kufika ku Yerusalemu wakumwamba (18-29)
13