“Tawonani! Ndikupanga Zinthu Zonse Zatsopano”
Liri pamwambali liri lonjezo lochokera kwa Mulungu lomwe linatengedwa monga mutu wa kabroshuwa katsopano. Kodi lonjezolo limatanthauzanji kaamba ka ife? Kodi lidzakwaniritsidwa motani, ndipo liti?
Pezani mwakuŵerenga chofalitsidwa chabwino kwambiri, cha masamba 32. Chidzatumizidwa kwa inu pamodzi ndi mabroshuwa a Boma Limene Lidzabweretsa Paradaiso ndi Sangalalani ndi Moyo pa Dziko Lapansi Kosatha!, kokha pa K7.20.
Chonde nditumizireni, mutalipiriratu positi, timabroshuwa titatu “Tawonani! Ndikupanga Zinthu Zonse Zatsopano,” Boma Limene Lidzabweretsa Paradaiso, ndi Sangalalani ndi Moyo pa Dziko Lapansi Kosatha! Ndatsekeramo K7.20.