Tsamba 2
NKHONDO m’zaka za zana lathu lino zatenga chifupifupi mazana mamiliyoni angapo. Kuŵaŵa, chisoni, ndi kuvutitsidwa komwe izi zapangitsa nkosaneneka. Kodi ndimotani mmene opulumuka, ponse paŵiri asilikali ndi anthu wamba, akhalira okhoza kuchita nazo? Kodi ndichiyembekezo chotani chimene chiripo cha dziko lopanda nkhondo, dziko limene silidzakumananso ndi zipsyera zoterozo?
[Chithunzi patsamba 2]
Opulumuka ku kuvulaza kwankhanga pa Chisumbu cha Eniwetok mu Marshalls, 1944
[Mawu a Chithunzi]
Official U.S. Coast Guard Photo