Tsamba Lachiŵiri
“Kukumana, kwankhalwe kokhetsa mwazi pakati pa ochemerera a ku Britain ndi a ku Italy . . . kunasiya chifupifupi 38 atafa ndipo 350 atavulazidwa.”
“Gulu la anthu linawukira apolisi, kuponya mabomba a petulo, kufunkha m’mashopu ndi kugwetsa magalimoto.”
“Kumenyana kunawuka m’baŵa. Mabotolo anaponyedwa, mipeni inasololedwa ndipo nkhondo yopanda mwini inabuka.”
“Kulimbana ndi apolisi, magalimoto anagwetsedwa, mazenera anaswedwa, alendo anamenyedwa ndi kupakidwa malovu.”
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
European Cup, Brussels, Belgium, 1985, Reuters/Bettman News photos
[Mawu a Chithunzi patsamba 5]
Cover Photo: J. L. Swider/H. Armstrong Roberts