Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g90 7/8 tsamba 2-5
  • Tsamba 2

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Tsamba 2
  • Galamukani!—1990
Galamukani!—1990
g90 7/8 tsamba 2-5

Tsamba 2

KUGWIRITSIRIDWA ntchito kwa zinyama m’kufufuza kwamankhwala kumadzutsa nkhani za mwambo ndi makhalidwe zimene zimasonkhezera malingaliro a anthu m’njira zosiyanasiyana. Asayansi amanena mopanda chitsimikizo kuti kupita patsogolo kwakukulu m’mankhwala kukanakhala kosatheka popanda kugwiritsira ntchito zinyama. Wina anati: “Ngati sitidali okhoza kupanga kufufuza pa zinyama, pamenepo tikanapululutsidwiratu.”

OCHILIKIZA nyama amachitira chifundo kulakwira kuyenera kwa nyama ndi kuvutika limodzi ndi kupanda ulemu kochitiridwa pa zinyama mamiliyoni ambiri zogwiritsiridwa ntchito m’kuyesera. Iwo amanena mopanda chitsimikizo kuti tsopano pali zinthu zolowa m’malo zinyama, monga ngati zitsanzo za makompyuta ndi minyewa yopangidwa, imene asayansi ayenera kugwiritsira ntchito.

PALI makani ovomereza ndi kutsutsa mbali ziŵiri zonsezo. Tikusanthula nkhanizo m’mipambo yathu yotsegulira, tikumalingalira choyamba lingaliro lasayansi pa kufufuza nyama.

[Mawu a Chithunzi patsamba 5]

Chithunzi chapachikuto: Courtesy of The Pedigree Mutt Pet Shop

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena