“Tawonani! Ndikupanga Zinthu Zonse Zatsopano”
Lomwe liri pamwambalo ndi lonjezo lochokera kwa Mulungu lomwe latengedwa kukhala mutu wa broshuwa yokongola. Kodi lonjezolo likutanthauzanji kwa inu? Kodi lidzakwaniritsidwa motani, ndipo liti?
Inu mungadziwonere nokha mwakuŵerenga bukhu lokongolali lamasamba 32. Ngati mukufuna kulandira kope, chonde dzazani ndi kutumiza kapepala komwe kali pansipa.
Ndingakonde kulandira broshuwa yamasamba 32 yakuti “Tawonani! Ndikupanga Zinthu Zonse Zatsopano” (Kunja kwa Zambia, lemberani nthambi ya Watch Tower ya kumaloko kaamba ka chidziŵitso. Onani tsamba 4.)