Tsamba 2
Tonsefe tinavutika kapena kuwonapo munthu wina amene timakonda akuvutika. Ndithudi, mbiri ya anthu njodzala ndi zolembera za kuvutika kwa anthu kochititsidwa ndi zinthu zosiyanasiyana. Kodi nchifukwa ninji Mulungu wakulola kumeneku kwanthaŵi yaitali chotere? Kodi kuvutikaku kudzatha konse?