Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g90 10/8 tsamba 32
  • Kodi Munayamba Mwaganizapo Kuti?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Munayamba Mwaganizapo Kuti?
  • Galamukani!—1990
Galamukani!—1990
g90 10/8 tsamba 32

Kodi Munayamba Mwaganizapo Kuti?

◻ Kodi Mulungu amalingaliranji za chisudzulo?

◻ Kodi Baibulo limavomereza dama kapena kugonana kwa ofanana ziŵalo?

◻ Kodi nchifukwa ninji Mulungu walola kuvutika?

◻ Kodi iye anafunadi kuti dziko likhale tere?

◻ Kodi mtsogolo mwasunganji?

Mmodzi wa Mboni za Yehova angakonde kukuchezerani ndi kukuthandizani kupeza mayankho a m’Baibulo ku mafunso oterowo. Mboni za Yehova zimapereka malangizo aumwini ndi apagulu ochokera m’Baibulo popanda malipiro.

Motero ngati mungafune kuchezeredwa ndi munthu panyumba panu kapena pamalo ena oyenerera, tidzakhala osangalala kupanga makonzedwe. Mudzathandizidwa kupeza osati kokha mayankho ku mafunso anu a m’Baibulo komanso mayankho ku mavuto alerolino amene angathetsedwe mwakugwiritsira ntchito malamulo amakhalidwe abwino a Baibulo. Kuti mupindule inu eni ndi utumiki umenewu, tangodzazani chidziŵitso chofunikacho chofunidwa pansipa ndikuchitumiza ku keyala ili pansiyi.

(Kunja kwa Zambia, lemberani nthambi ya Watch Tower ya yakwanuko. Onani tsamba 4.)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena