Zisonyezero za Volyumu 34 ya Galamukani!
ACHICHEPERE AKUFUNSA KUTI
Amai ndi Atate Ali Osaphunzira—Kodi Ndingawalemekeze Bwanji? 1/8
Kholo Lomwe Linachoka Panyumba, 11/8
Kodi Nchifukwa Ninji Izi Zikuchitika ku Thupi Langa? 2/8
Kodi Nchiyani Chikuchitika ku Thupi Langa? 2/8
Kodi Ndibatizidwe? 4/8
Kodi Ndimotani Mmene Ndingathetsere Kusungulumwa Kwanga? 1/8
Kodi Ndine Wokonzeka Kubatizidwa? 4/8
Kodi Ndingasankhe Motani Kanema Yabwino? 8/8
Kodi Ndiyenera Kudziperekeranji Kaamba ka Ena? 6/8
Kodi Nkuliphunziriranji Baibulo? 10/8
Kodi Ziri Nkanthu Akanema Amene Ndimawonerera? 8/8
Kudzikometsera, 6/8
Kukhala ndi Kholo Limodzi, 7/8
Kukhala ndi Pakati kwa Achichepere, 5/8
Kupanga Kupita Patsogolo Kwauzimu, 10/8
Kupeŵa Matsenga, 3/8
Makolo Amandichititsa Manyazi, 3/8
Makolo Anga Akulekana—Kodi Ndichitenji? 9/8, 11/8
Masitayelo ndi Mipikisano ya Kukongola, 1/8
Nchifukwa Ninji Kudzimva Wopanda Chisungiko? 5/8
Ntchito Yapambuyo Poŵeruka Kusukulu, 12/8
Zopakapaka, 7/8
CHIPEMBEDZO
Chifukwa Chimene Mulungu Analola Kuvutika, 10/8
Kukongola Kwamuyaya kwa Chipembedzo Chowona, 1/8
Kulekana Kwatsopano, 7/8
Mafunso Omwe Amafunikira Kuyankhidwa, 10/8
Nchifukwa Ninji Pali “Kuda Nkhaŵa Kwakukulu,” 7/8
Nchifukwa Ninji Pali Kugaŵanikana? 7/8
Tchalitchi cha Chikatolika mu Spanya—Kodi Nchifukwa Ninji Vutolo? 3/8
Tchalitchi cha Chikatolika mu Spanya—Kugwiritsira Ntchito Ulamuliro Molakwa, 3/8
Tchalitchi cha Chikatolika mu Spanya—Ulamuliro ndi Mwaŵi, 3/8
Tchalitchi cha Chikatolika mu Spanya—Zitsutsano, 3/8
Ufulu, 10/8
CHUMA NDI NTCHITO YOLEMBEDWA
Ngongole! Kuloŵamo—Kutulukamo, 2/8
LINGALIRO LA BAIBULO
Angelo, 3/8
Ayuda Anthu Osankhidwa a Mulungu? 7/8
Hanukkah—Kodi Ndiyo “Krisimasi” Yachiyuda? 12/8
Kodi Ndiliti Pamene Moyo wa Munthu Umayambika? 10/8
Kodi Sayansi Yapangitsa Baibulo Kukhala Lachikale? 8/8
Korona, 6/8
Kudzipha—Kodi Pali Chiukiriro? 9/8
Mankhwala Ogodomalitsa Ngosangulutsira—Chifukwa Ninji Ayi? 11/8
Mdyerekezi Alikodi? 1/8
Pemphero m’Maseŵera, 5/8
Tchimo Loyambirira, 4/8
MAIKO NDI ANTHU
Thanthwe la Gibraltar, 1/8
Ulendo wa Pamtsinje wa Chobe (South Africa), 8/8
MAUNANSI A ANTHU
Anthu a Fuko Lina—Kodi Mumaŵalingalira Motani? 12/8
Apongozi—Kodi Chimachititsa Vutolo Nchiyani? 3/8
Apongozi—Kusangalala Unansi Wabwino, 3/8
Apongozi—Mkangano Wakalekale, 3/8
Kupyolera m’Maso Amwana, 2/8
Makhalidwe Abwino Kubwereranso? 6/8
Mapindu a Makhalidwe Abwino Amene Amabweretsa Chimwemwe, 6/8
Zomwe Timadziŵa Ponena za Fuko, 12/8
MBONI ZA YEHOVA
Adokotala ndi Mboni Zodwala, 12/8
Chivomerezo cha Oŵerenga Bukhu la Young People Ask, 9/8
Ubale Wapadziko Ngotsimikizirika, 12/8
NKHANI ZOSIYANASIYANA
Achichepere Amakono—Akumana Ndi Zitokoso za m’ma 1990, 9/8
Achichepere Amakono—Chithunzi cha Padziko Lonse, 9/8
Achichepere Amakono—Zitokoso Zimene Amakumana Nazo, 9/8
‘Chizoloŵezi Choipachi Chakusuta Fodya,’ 8/8
Choipitsitsa Kuposa AIDS, 2/8
Dziko Latsopano Lopanda Mavuto, 10/8
Khutu—Wolankhulira Wamkulu, 2/8
Kodi Ndimphatso ya Moyo Kapena Mpsopsono wa Imfa? 11/8
Kodi Nthaŵi Zonse Mumachedwa? 1/8
Mabuku Aulere, 9/8
Madzi Amtengo Wapatali Kwenikweni m’Dziko, 11/8
Maphindu Osintha ndi Kupita kwa Mbiri, 6/8
Mmene Mungachitire Zambiri mu Nthaŵi Yochepa, 6/8
Moyo Kunja kwa Dziko Lapansi—Kodi Kuli Aliyense Kunja Kumeneko? 4/8
Zamoyo Zakuthambo—Kodi Ziri Kuti? 4/8
Zamoyo Zakuthambo—Kupeza Yankho, 4/8
Zamoyo Zakuthambo—Loto Lakalekale, 4/8
NYAMA NDI ZOMERA
Kodi Nchiyani Chimene Chinachitika kwa Madinosaur? 2/8
Kodi Ndani Amene Akupha Nkhalango Zamvula? 4/8
Kodi Nkhalango Ziri ndi Mtsogolo? 4/8
Kodi Nkusungiranji Nkhalango Zamvula? 4/8
Kufufuza Nyama—Dalitso Kapena Temberero? 7/8
Kufufuza Nyama—Kawonedwe Kolinganizika, 7/8
Kufufuza Nyama—Zivomerezo Zachiwawa, 7/8
Kupeza ‘Zokwawa Zazikulu’ Zakale, 2/8
Mawonekedwe ndi Maukulu Osiyana a Madinosaur, 2/8
“Pitani ku Nyerere,” 6/8
Walrus ndi Malonda a Mankhwala Ogodomalitsa, 2/8
Wosangalatsa Wofiirayo ndi Nyimbo Yosangalatsa, 3/8
ULAMULIRO WA ANTHU UYESEDWA
“Anthufe,” 10/8
‘Boma Lolamulidwa ndi Abwino,’ 9/8
Kufunafuna Utopia kwa Ndale Zadziko, 11/8
Kulamulira kwa Munthu Kufikira Mapeto Ake, 12/8
Mafumu, Amakwera ndi Kugwa, Mofanana ndi Nyenyezi, 9/8
Malaya Akuda ndi Maswastika, 11/8
Mphamvu Zopanda Malire—Dalitso Kapena Temberero? 10/8
Nsanganizo Wandale Zadziko wa Chitsulo ndi Dongo, 11/8
Ulamuliro wa Anthu Uyesedwa Pamiyeso— Chifukwa Ninji? 8/8
UMOYO NDI MANKHWALA
Chikhulupiriro Chinandithandiza Kuyang’anizana Ndi Opareshoni ya Ubongo, 5/8
Kodi Kugulitsa Mwazi Kuli Bizinesi Yaikulu, 11/8
Kodi Kuthiridwa Mwazi Ndiko Mfungulo Yopulumukira? 11/8
Kodi Tingakhale kwa Utali Wotani? 5/8
Kufunafuna Moyo Wautali, 5/8
Kukhala ndi Khunyu, 7/8
Makanda, Mwazi, ndi AIDS, 7/8
Minkhole Yopepuka ya Fodya, 10/8
Mtengo wa Kusawona Mtima (Nkhani Yamwazi), 10/8
Mtundu Woipitsitsa wa Kuipsya Mwana (Kusuta), 1/8
Pamene AIDS Siirinso Chiwopsezo, 3/8
“Sindidzayendanso,” 9/8
ZOCHITIKA ZA DZIKO NDI MAKHALIDWE
Achichepere—Zitokoso za m’ma 1990, 9/8
Ana Opanda Kokhala—Kodi Nchifukwa Ninji Kuli Kovuta Kuthandiza? 1/8
Ana Opanda Kokhala—Kodi Ndani Ali ndi Liŵongo? 1/8
Ana Opanda Kokhala—Kodi Pali Yankho? 1/8
Dziko Laudongo—Tikulifunadi, 5/8
Kodi Tifunikiradi Boma? 8/8
Kuipitsa—Kodi Ndani Akukuchititsa? 5/8
Kumwerekera ndi Crack—Kodi Pali Njira Yokuthetsera, 8/8
Kumwerekera ndi Crack—Mliri Wake wa Chiwawa, 8/8
Kumwerekera ndi Crack—Tsoka kwa Ana Osabadwa, 8/8
Kutembenuzira Chisamaliro pa Boma, 8/8
Malo Otizinga Omanyonyotsoka, 2/8
Mapeto a Kuipitsa Ali Pafupi, 5/8
Ma 1990—Zaka Khumi Zosatsimikizirika, 8/8
Mfuti—Dziko Lopanda Izo, 6/8
Mfuti—Njira ya Imfa, 6/8
Mfuti—Njira ya Moyo, 6/8
Mfuti—Sizaamuna Okha, 6/8