Tsamba 2
Miseche Mmene Mungapeŵere Kuvulazidwa 3-10
Miseche ingakhale yopereka chidziŵitso, yosangalatsa, yodzetsa mpumulo, koma ingakhalenso yolipsira ndi yowononga. Kodi nchifukwa ninji kaŵirikaŵiri imasanduka kukhala chinachake chovulaza? Kodi ichi chingapeŵedwe motani?
Kodi Ndiyenera Kuphatikana ndi Gulu? 14
Kodi nchifukwa ninji ambiri amaphatikana ndi magulu? Pali njira yabwinopo yopezera ubwenzi.