Tsamba 2
Akazi Ayenera Kupatsidwa Ulemu 3-17
Kwa zaka zikwi zambiri, akazi achitiridwa nkhanza, kuvutitsidwa, ndi kutsenderezedwa. Tsopano zinthu ziyamba kuwakhalira bwino. Kodi nchifukwa ninji akazi ayenera kupatsidwa ulemu m’zitaganya zonse? Kodi amuna angawongokere motani m’kuchita kwawo ndi akazi?
Kodi Ndingalimbe Mtima Motani Kuti Ndikhale Wosiyana ndi Ŵena? 18
Chitsenderezo cha ausinkhu wawo chimasonkhezera achipepere mwamphamvu. Kodi angakhale motani olimba mtima kuti apirire ndi kukhala osiyana ndi ŵena?