Tsamba 2
AIDS MU AFIRIKA—Kodi Idzatha Motani? 3-11
Zaka zoŵerengeka zapitazo kunalingaliridwa kuti mliri wa AIDS unali kuyambika mu Afirika. Koma kodi uwo wafika pati tsopano? Kodi zimenezi zikutanthauzanji kumaiko ena? Mlembi wa Galamukani! mu Afirika akupereka mayankho ake.
Kholo Chidakwa—Kodi Ndingalake Motani? 17
Achichepere amene amaleredwera m’banja limene kholo liri chidakwa amayanganizana ndi chitokoso chachikulu. Kodi iwo angachilake motani?
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
WHO/E. Hooper