Tsamba 2
Kodi Ndewu m’Banja Zidzatha Konse? 3-14
‘Ngakhale antchito athu amaukiridwa pamene amka kukafufuza ndewu m’banja,’ akusimba motero mtsogoleri m’zamakhalidwe a anthu. Kodi nchifukwa ninji banja liri landewu chotero? Kodi nchiyani chimene chingachitidwe kuyesa kuiletsa? Bwanji ngati simungathe? Kodi idzatha konse?
Kodi Cholakwika Nchiyani ndi Nyimbo Zanga? 18
Achichepere amafuna kuimba nyimbo zawozawo. Koma ena angatsutse. Kodi lingaliro lachikatikati nlotani pankhani imeneyi?