Tsamba 2
Sayansi Kodi Ingakwaniritse Zosoŵa Zathu? 3-8
Mavuto amene akuyang’anizana ndi dziko tsopano ayenera kuthetsedwa ngati mtundu wa anthu uti upulumuke tsoka. Powona kuti zaka za zana la 21 zayandikira, nali funso, Kodi kufunafuna chowonadi cha sayansi kwa mtundu wa anthu kudzakhoza kuchita ndi mavuto ameneŵa?
Kodi Ndimotani Mmene Ndingasungire Nyimbo m’Malo Ake? 9
Musalole nyimbo kukhala chinthu chofunika koposa m’moyo wanu. Sangalalani nazo, koma zisungeni m’malo ake