Tsamba 2
Dziko Lopanda Matenda—Kodi Nlotheka? 3-10
Kwa zaka mazana ambiri anthu avutika ndi matenda. Kodi idzafika nthaŵi pamene matenda onse adzathetsedwa?
Kodi Ndani Akhoza Kundithandiza Kuthetsa Mavuto Anga? 26
Achichepere amayang’anizana ndi zovuta zambiri masiku ano. Kodi nkuti kumene angapeze chithandizo?