Tsamba 2
Mizinda Yathu Kuyesayesa Kwake Kukhalapobe 3-12
Polingalira za upandu ndi kuchulukitsitsa kwa anthu, kodi nchifukwa ninji anthu mamiliyoni ambiri amasankha kukhala m’mizinda? Kodi ndimavuto ena otani amene akukantha anthu okhala m’mizinda lerolino?
Moyo Wapaŵiri—Kodi Ndani Ayenera Kudziŵa? 30
Kungakhale kosavuta kwa achichepere ena kunamiza makolo awo—koma kodi mphotho ya kukhala ndi moyo wapaŵiri njotani?