Tsamba 2
Chitokoso cha Kusamalira Makolo Okalamba 3-10
Anthu owonjezerekawonjezereka akukakamizika kusamalira makolo okalamba. Kodi zimenezi zingachitidwe motani mwachipambano?
Kuseŵera ndi Chisembwere—Kodi Kuli ndi Chivulazo Chotani? 16
Kodi ndikhalidwe lotani limene lili losayenera kulinga kwa wosiyana naye ziŵalo?
Kodi Nkusudzula kwa Mtundu Wotani Kumene Mulungu Amada? 29
Kodi pali chisudzulo cha mtundu uliwonse chimene Mulungu amalola?
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
Historic Costume in Pictures/ Dover Publications, Inc., New York