Tsamba 2
Kodi Mukudziŵa Chimene Mwana Wanu Akuseŵera Nacho? 3-10
Zoseŵeretsa zopanda upandu zakhala mbali ya miyoyo ya ana kwa zaka mazana ambiri. Koma kodi zoseŵeretsa za lerolino zili zopanda upandu nthaŵi zonse? Kodi zoseŵeretsa zingakhale zikuyambukira motani ana anu?
Malangizo Ofunika a Kuyamwitsa Bere 10
Kodi nchifukwa ninji makanda oyamwitsidwa bere ndiwo odyetsedwa bwino koposa? Kodi ndimotani mmene amayi angakhalire ndi chipambano cha kuyamwitsa bere?