Tsamba 2
Kodi Mumapsa ndi Ntchito? 3-10
Kupsinjika ndi ntchito kukuchititsa anthu ambiri kupsa ndi ntchito. Anakubala osamalira ana amapsa ndi ntchitoyo. Koma kodi kupsa ndi ntchito nchiyani? Kodi inu mukuonekera kuti mungapse ndi ntchito? Kodi pali njira yopeŵera kapena yolimbanirana ndi zimenezo?
Kusamalira Ovutika ndi Tsoka la ku Rwanda 12
Taŵerengani za mmene Mboni za Yehova zaperekera chithandizo kwa othaŵa ku Rwanda.
Tchalitchi cha Katolika mu Afirika 18
Mabishopu akuyang’anizana ndi mkhalidwe wa kuphana kwa Akatolika zikwi makumi ambiri m’Rwanda ndi Burundi.
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
Jerden Bouman/Sipa Press