Tsamba 2
Ana Osoŵa—Kodi Tsokalo Lidzatha Liti? 3-13
Chaka chilichonse kuzungulira padziko lonse, pamakhala zikwi mazana ambiri za ana osoŵa. Kodi nchiyani chimene chimawachitikira? Kodi nchiyani chimene chingachitidwe pa zimenezi?
Mpunga—Kodi Mumakonda Wophika Kapena Wosaphika? 16
Njira imene amaphikira mpunga kumaiko Akumadzulo njosiyana ndi mmene amaukonzera ku India. Suzumirani ndi chidwi m’khalidwe la kumalo ena.