Tsamba 2
Kodi Munthu Adzakhoza Kulimbana ndi Masoka? 3-9
Madzi osefukira ku Ulaya! Chivomezi ku Japan! Mikuntho! Kuphulika kwa mavolokano! Zikuchita ngati kuti nkhondo ya munthu ndi masoka siidzatha konse. Kodi maboma akuchitapo chiyani? Kodi Mulungu adzachitapo chiyani?
Kodi Ndingakhaledi Bwenzi la Mulungu? 29
Ena amene analakwa ndipo aganiza kuti ali osayenera amakayikira ngati zimenezo zili zotheka.