Tsamba 2
1945-1995—Kodi Taphunzira Chiyani? 3-14
Papita zaka 50 chiyambire kutha kwa Nkhondo Yadziko II. Kodi anthu apita patsogolo m’njira zotani? Kodi zopinga zina za kupita patsogolo nzotani? Kodi tili ndi chiyembekezo chotani cha boma langwiro?
Kuvutitsidwa ndi Amuna Kapena Akazi—Kodi Ndingadzitetezere Motani? 30
Achichepere ambiri amavutitsidwa ndi amuna kapena akazi. Kodi angadzitetezere motani?
[Mawu a Chithunzi pamasamba 2, 4]
Masamba 2 ndi 3: Churchill, Roosevelt ndi Stalin ku Yalta: UPI/Bettmann; Galimoto: Index Stock Photography; Mkazi: Index Stock Photography; Mwamuna pafoni: Index Stock Photography; Kumbuyo: Chithunzi cha U.S. Army
[Mawu a Chithunzi patsamba 1]
Pachikuto: Chithunzi cha USAF