Tsamba 2
Ulova—Chouthetsera Chake Chilipo 3-11
Pali anthu pafupifupi 820 miliyoni amene sagwira ntchito kapena ogwira ntchito ya masiku ochepa padziko lonse. Polingalira za mabanja awo, kodi mungaganize za nsautso ndi kuvutika kumene zimenezi zimachititsa? Kodi nchiyani chimene chimachititsa ulova? Kodi padzakhala chouthetsera chake?
Nkhondo ya Munthu ndi Tizilombo ta Matenda 21-29
Kodi nthendazi zikuchokera kuti? Kodi nchifukwa ninji tizilombo ta matenda tikuoneka ngati tikupambana? Kodi pali mankhwala ake?
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
Vairasi pamwamba pa masamba 21, 22, ndi 28: CDC, Atlanta, Ga.