Tsamba 2
Pamene Sikudzakhalanso Kuvuta Akazi! 3-10
Ntchito yakhala chizunzo kwa akazi ambiri amene amagwira ntchito. Kuvutidwa konyazitsako kumaphatikizapo mawu otukwana ndi onyansa. Zoyesayesa za eni ntchito ndi kupita ku makhoti kwatulutsa zabwino. Akazi achikristu apeza kuti kumathandiza kutsatira mapulinsipulo a Baibulo pakavalidwe kawo ndi khalidwe.
Ntchentche ya Kambalame—Ndi Tsoka la Afirika Kodi? 11
Ntchentche ya kambalame ndi mdani wamphamvu, koma kodi njoipa pa zonse?
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
©Martin Dohrn, The National Audubon Society Collection/PR