Tsamba 2
Kodi kusamvana Kuyenera Kutigaŵanitsa? 3-8
Mosasamala kanthu za chidziŵitso chokulirapo cha chikhalidwe cha anthu ena, chimene TV ndi maulendo osavuta zapereka, anthu adakasonkhezeredwabe ndi kukondera ndi tsankho. Kodi zopinga kulankhulana komasuka ndi kumvana zomwe zidakalipo zingachotsedwe?
Masamba a Chinangwa—Chakudya Chatsiku ndi Tsiku cha Mamiliyoni Ambiri 20
Ngakhale kuti mitundu ina njaululu, chomera chimenechi ndi chimene ambiri mu Afirika amadalira. Kodi amachikonza motani? Kodi nchiyani chimachititsa kuti chikome kwambiri?
Ma UFO—Kodi Ali Amithenga Ochokera kwa Mulungu? 26
Anthu ena amati anakumanapo ndi zamoyo zakuthambo. Kodi zifukwa zake nzotani? Kodi Baibulo limati chiyani?
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
Mountain High Maps® Copyright © 1995 Digital Wisdom, Inc.