Tsamba 2
Zotsatirapo za Kusintha Maganizo pa Zakugonana 3-10
Nthaŵi zonse kugonana ndi ena kunja kwa ukwati kwawonongetsa kwambiri ulemu, thanzi, ndi unansi wa munthu ndi Mulungu. Koma kodi kuopa AIDS kwasintha maganizo a anthu?
Nkulamuliriranji Mkwiyo Wanu? 11
Mofanana ndi volokano yophulika, mkwiyo wosalamulirika ungakuvulazeni inuyo ndi ena.
Singapore—Ngale Yowonongeka ya Asia 25
Kodi kukongola kwa Singapore nkolingana ndi mbiri yake pa zoyenera za anthu?
[Mawu a Chithunzi patsamba 5]
Sauli Afuna Kupha Davide/The Doré Bible Illustrations/Dover Publications, Inc.