Tsamba 2
Kodi Ndani Adzapulumutsa Nyama Zathu? 3-11
Dziŵani chifukwa chake nyama zikwi zambiri zikusoloka. Kodi zimenezi zingapewedwe motani?
Kodi Galu Wanu Sangavulaze Ana? 12
Kodi mungatani kuti mutetezere ana anu kwa galu waukali? Kodi imeneyo ndi ntchito ya mwini galu yekha?
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
Kamba: Zoological Parks Board of NSW