Tsamba 2
Thandizani Ana Anu Kukula Bwino 3-11
Kuti ana akule bwino, afunikira malo olimbikitsa malingaliro abwino. Kodi makolo angatani kuti apereke malowo?
Bwanji Amaimba Ine Mlandu Nthaŵi Zonse? 20
Kodi zimachitika kuti chilichonse chomwe chalakwika, amaimba inu mlandu? Kodi mungachitenji pamene akudzudzulani mosayenera?
Khalidwe Loipa—Kodi Mtengo Wake Ngwaukulu Motani? 26
Anthu ambiri amawagoneka m’chipatala chifukwa cha matenda ndi kuvulala komwe akanapeŵa. Chochititsa? Khalidwe langozi.