Tsamba 2
Chimene nkhondo zimachita kwa Ana 3-11
Nchifukwa ninji ana amalembedwa ntchito yausilikali? Kodi nkhondo yawasakaza motani? Komabe, nchifukwa ninji tingakhale ndi chikhulupiriro kuti ana amakonowa adzakhala ndi mtsogolo mwabwino?
Kutengapo Phunziro pa Mphika wa Mafuta 12
Nkhani yolimbikitsa ya Kurt Hahn ikusonyeza phunziro lothandiza limene tingatengepo pa mphika wa mafuta.
Nchifukwa Ninji Mbale Wanga Amamuikako Nzeru Kwambiri? 17
Nchiyani chomwe mungachite ngati makolo anu aoneka kuti akukondera mbale wanu?
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
Nanzer/Sipa Press
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
Masamba 1, 3, 4, ndi 7: Chithunzithunzi cha U.S. Navy