Tsamba 2
Nkhanza kwa Zaka Zana Limodzi—Kodi Ino Ndiyo Nthaŵi Yoiŵala? 3-11
Nkhanza zapha anthu mamiliyoni ambiri. Kodi ndani angalonjeze kuti sizidzachitikanso?
Nchifukwa Chiyani Sinditha Kumvetsera? 12
Kodi mumavutika kusumika maganizo anu pazinthu? Ngati zili choncho, nanga mungatani?
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
Mtsikana wovulazidwa wa ku France: U.S. Navy photo
Mitembo ya anthu a ku Rwanda othaŵa kwawo: UN PHOTO 186809/J. Isaac