Zisonyezero za Voliyumu 79 ya Galamukani!
ACHINYAMATA AKUFUNSA
Akukana Ukwati Wanga, 2/8
Choonadi Kukhala Changachanga, 11/8
Kukhoza Kusukulu, 4/8
Kutamanda Mtundu Wako, 3/8
Madansi a Rave, 1/8
Mnzanga Azindipatsa Mpata, 5/8
Ndikukhala Wopanda Makolo, 12/8
Nditsanzire Yani? 6/8
Ndizimvetsera Mwachidwi, 10/8
Ndizipeza Ndalama, 9/8
Sasonyeza Kuti Amandifuna, 7/8
Sinditha Kumvetsera, 8/8
CHIPEMBEDZO
Yesu—Kale ndi Tsopano, 12/8
CHUMA NDI NTCHITO
Kodi Ntchito Yanu Sikusangalatsani? 1/8
LINGALIRO LA BAIBULO
Chaka cha 2,000, 5/8
Kodi Ziŵanda Zilipodi? 4/8
Kuimba Mlandu Satana? 9/8
Kuseŵera Kokopana, 7/8
Kuzunza Nyama—Kodi Nkulakwa? 11/8
Lumbiro La Kusakwatira, 6/8
Maphunziro Akusukulu, 3/8
Miyala Idzagunda ndi Kuwononga Dziko? 12/8
Mmene Mumapesera ndi Mmene Mumavalira, 8/8
Mungamuope Bwanji Mulungu Wachikondi? 1/8
Ubwino Wakukhala Panokha, 10/8
Umodzi Wachikristu, 2/8
MAIKO NDI ANTHU
“Njanji Yopanda Phindu,” 10/8
Njira Zisanu Zowongolera Moyo Wanu, 6/8
MAUNANSI A ANTHU
Kupweteka Mtima Polola Mwana Kuchoka Panyumba, 2/8
MBONI ZA YEHOVA
Atolankhani a ku Russia Athokoza, 3/8
European Court, 1/8
Kulimba Mtima pa Chiopsezo cha Anazi, 7/8
NKHANI ZA MOYO WA ANTHU
Kusankhapo Pakati pa Atate Aŵiri, 6/8
Ndinalimbikitsidwa (H. Henschel), 3/8
Ulendo Wanga Wautali (W. Meas), 5/8
SAYANSI
Kodi Anthufe Ndife Chiyani? 7/8
UMOYO NDI MANKHWALA
AIDS, 11/8
Akukana Magazi, 10/8
Matenda a Alzheimer, 10/8
Kumwa Mankhwala Panokha, 7/8
Kupsinjika Maganizo, 4/8
Kuvutika ndi Mantha, 8/8
Madzi ndi Thanzi Lanu, 4/8
Mutha kusiya, 12/8
Opaleshoni Popanda Mpeni Wake, 3/8
Opaleshoni Yopanda Kuika Magazi, 9/8
Stroko! 2/8
Chifuwa cha TB, 1/8
ZINYAMA NDI ZOMERA
Dengue, 8/8
Mitengo Yokongola Yakalekale, 11/8
Ngale za m’Miyamba ya Afirika, 8/8
Nkhalango Zamvula, 5/8
Tsankho Lolekanitsa Anthu M’magulu, 3/8
ZOCHITIKA ZA DZIKO NDI MIKHALIDWE YAKE
Achinyamata ali ndi Tsogolo Lotani? 9/8
Akazi, 4/8
Anthu Onse Adzakhala Okondana? 11/8
Kuchuluka kwa Chidziŵitso, 1/8
Magulu Aupandu, 5/8
Mmene Nyengo Idzakhalira Mtsogolo, 6/8
Mphamvu ya Osatsa Malonda, 9/8
Nkhanza kwa zaka Zana Limodzi? 8/8
Ufulu Wachibadwidwe, 12/8
Umphaŵi, 6/8
Upandu, 3/8
ZOSIYANASIYANA
Chinenero Chochita Kuona ndi Maso, 9/8
Gutenberg, 11/8
Moyo Wotetezereka Kosatha, 10/8
Pamene Kufa Kumakhaladi Kufa, 7/8
Tinathaŵa Mabomba, 3/8