Tsamba 2
Pamene Mwamuna Kapena Mkazi Akhala Wosakhulupirika 3-12
Kodi ena am’banjamo zimawakhudza bwanji? Kodi wina ayenera kuyesa kubwererana ndi mnzake wachigololoyo? Kodi kungakhale kwanzeru kuganiza za chisudzulo?
Phiri la Sinai—Mwala Wokongoletsa Chipululu 16
Yenderani Phiri la Sinai lalero, mwinadi n’lomwelo limene Mose anakwera
Pamene Anatitengera ku Ukapolo ku Siberia! 20
Ŵerengani za mmene banja lina linapiririra zaka za ukapolo ku Siberia, ndipo phunzirani mmene kukhulupirira kwawo Mulungu kunawathandizira.
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
Pictorial Archive (Near Eastern History) Est.