Tsamba 2
Kodi Kuopa Nyukiliya Kwatha? 3-11
Pamene mkangano wapakati pa dziko la United States ndi Russia unatha, anthu ambiri anasangalala kuti mtundu wa anthu sudzaopsedwanso ndi nkhondo ya nyukiliya. Komabe nkhani zotsatirazi zikulongosola zina mwa zifukwa zimene tinganenere kuti zida za nyukiliya zidakali kuopseza anthu kwambiri kuposa mmene anthu ambiri amaganizira.
Kutumikira Mulungu Poyang’anizana ndi Imfa 18
Kwa zaka zambiri anapirira kuzunzidwa ndiponso anatsekeredwa m’ndende ndi kutumizidwa ku ukaidi. Ŵerengani nkhani yolimbikitsa ya munthu wa ku Afirika ameneyu.
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
Bomba lophulika lili pachikutopo: UNITED NATIONS/PHOTO BY SYGMA