Zamkatimu
November 8, 2002
Kodi Mliri Wopulula Anthu wa EDZI Udzagonjetsedwa?
Edzi ndi mliri wa padziko lonse. Komabe, posachedwapa ku South Africa mliriwu wavuta kwambiri. Kodi pali njira yougonjetsera?
3 “Sipanakhaleko Mliri Wosakaza Kwambiri Chonchi N’kale Lonse”
8 Ngati Mliri wa Edzi Udzagonjetsedwe, Kodi Ungadzagonjetsedwe Bwanji?
12 Mmene Tinapulumukira Zoopsa Phiri Litaphulika N’kumatuluka Chiphalaphala!
19 Kodi Zamtendere Zikukayikitsa Tsopano?
20 Zipembedzo Zinakakumana ku Assisi Pofuna Mtendere
24 Kodi Ndani Adzabweretse Mtendere Wosatha?
28 Kukumananso Modabwitsa Patatha Zaka 30
32 Mayankho Othandiza a Mafunso Amene Mwakhala Mukufunsa!
Kodi Ndikufunika Telefoni ya M’manja? 16
Telefoni yothandiza imeneyi ili ndi poipira pake. Kodi tingatani kuti telefoni yam’manjayi tiigwiritsire ntchito bwino?
Kodi Mulungu Amanyalanyaza Zofooka Zathu? 26
Kodi zofooka zathu tingazigonjetse? Kodi tiyenera kutani?
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
Copyright Sean Sprague/Panos Pictures
AP Photo/Efrem Lukatsky
PA CHIKUTO: Alyx Kellington/Index Stock Photography