Zamkatimu
March 8, 2004
Kodi Nkhondo ya Nyukiliya Ingachitikedi?
N’chifukwa chiyani nkhondo ya nyukiliya ikutidetsabe nkhaŵa mpaka panopa? Kodi ndani angachititse nkhondo yotere? Nanga ingathe kupeŵedwa?
3 Kodi Nkhondo ya Nyukiliya Anthu Akuiopabe?
4 Kodi Nkhondo ya Nyukiliya Angaichititse Ndani?
8 Kodi Nkhondo ya Nyukiliya Anthu Angaipeŵe?
10 “Njira ya Anthu Pofunafuna Mulungu”
11 Zinyama Ndi Mphatso Yochokera kwa Mulungu
14 Ziweto Tifunika Kuziona Moyenera
18 Zinyama Zidzasangalatsa Anthu Mpaka Kalekale
23 Chomera Chopirira Modabwitsa
32 ‘Muli Nkhani Zothandiza Kwambiri’
Kuyendera Mathithi Ochititsa Kaso 24
Mathithi a Victoria Falls ndi amene amatengedwa kuti ndi malo aakulu kwambiri padziko lonse okhala ndi madzi otsetsereka kuchoka pamwamba. Adziŵeni bwino mathithi ameneŵa ndiponso mathithi ena paulendo wosaiwalika wa ku Zambia.
Kodi Kumwa Mowa Mwauchidakwa N’koipadi? 30
Anthu ambiri amaganiza kuti palibe vuto lililonse kumwa mowa mwauchidakwa mwa apo ndi apo. Kodi Baibulo limatipo bwanji pankhaniyi?
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
COVER: U.S. Department of Energy photograph; page 2: Explosion: DTRA Photo