Zamkatimu
October 2010
Kodi Mungakhulupirire Ndani?
Kodi pali munthu wina aliyense amene tingamukhulupirire masiku ano? Yankho la funso limeneli lingakudabwitseni kwambiri.
3 “ Anthu Asiyiratu Kukhulupirirana”
4 Kodi Alipo Amene Tingamukhulupirire?
6 Anthu Amene Mungawakhulupirire
10 Zidziweni Bwino Mbira Zam’mapiri
14 Kufufuza Njira Yolumikiza Nyanja ya Atlantic ndi Pacific Kumpoto kwa Dziko Lapansi
17 “Wotchi Yaikulu Kwambiri Padziko Lonse”
27 Mawu Amene Anthu Amagwiritsa Ntchito Zinthu Zikawavuta Panyanja
32 Kabuku Kothandiza Kwambiri kwa Ophunzira Baibulo
Matenda Amene Anavuta Kwambiri M’zaka za M’ma 1800 20
Werengani nkhaniyi kuti mumve mmene matenda a kolera anaphera anthu ku Britain m’zaka za m’ma 1800.
Kodi Ndingakwanitse Bwanji Zolinga Zanga? 24
Onani mmene kukhala ndi zolinga ndi kuyesetsa kuzikwaniritsa kungakuthandizireni kukhala wolimba mtima, kukhala ndi anzanu ambiri, komanso kukhala wosangalala.
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
© Mary Evans Picture Library