Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • te tsamba 191
  • Kanthu ka Banja Lanu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kanthu ka Banja Lanu
  • Kumamumvetsera Mphunzitsi Wamkuru’yo
  • Nkhani Yofanana
  • Mungapeze Buku Lina
    Mzimu Woyera—Mphamvu Yochirikiza Dongosolo Latsopano Likudza’lo!
Kumamumvetsera Mphunzitsi Wamkuru’yo
te tsamba 191

Kanthu ka Banja Lanu

Kuti mulinganize makambitsirano aulere a pa nyumba a Baibulo a mlungu ndi mlungu, onanani ndi mboni za Yehova m’chitaganya chanu kapena sonyezani chikhumbo chanu poitanitsa bukhu lapamwambapolo. Lembani kalata ku WATCHTOWER, mukumagwiritsira nchito keyala yochokera pa tsamba lotsatirapo.

• Coonadi Cimene Cimatsogolera ku Moyo Wamuyaya liri bukhu la banka lonse. Lingakuthandizeni ndi banja lanu kupeza kuzindikira kwangwe kwa ziphunzitso zonse zamaziko za Baibulo. Limapereka mayankho a Baibulo ku mafunso amene ana anu amafunsa ndi mafunso amene inu mosakaikira mumafunsa onena za moyo ndi tanthauzo lache. Pakati pa nkhani zokambitsiridwa pali yakuti “Kumaumanga Moyo Wabanja Wachimwemwe.”

• Mabanja mamiliyoni ambiri ali ndi bukhu limeneli Lachiwiri ku Baibulo, liri bukhu lofalitsidwa kwambiri m’dziko lakumadzulo. Bukhu la masamba 192, la chikuto cholimba limeneli lidzatumizidwa kwa inu litalipiridwiratu positi pa 20c.

• Ndiponso mboni za Yehova zimapereka programu yaulere ya mizeyi isanu ndi umodzi ya phunziro la Baibulo la pa nyumba. Kodi mungafune kuononga pafupifupi ora limodzi mlungu uli wonse kukambitsirana Baibulo?

• Kuti?—M’nyumba mwanu, kapena pa malo ena ali onse oyenera.

• Liti?—Pa nthawi yabwino kwa inu.

• Kodi Ndani Amene Angakhale m’Kukambitsiranako—?Kweni-kweni banja lanu lonse. Kapena, ngati mufuna, kungakhale kukambitsirana kochitidwa ndi inu nokha.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena