Mutu wa Kabuku Kano/Tsamba la Ofalitsa
M’tsogolo Mosungika—M’mene Mungamupezere
Ngati mukufuna moyo m’mikhalidwe yosungika, mudzapeza zimene zalongosoledwa m’kabukhu’ka kukhala zolimbikitsa kwambiri. Komabe, kuphatikiza pakukawerenga kwanu, tikukhulupirira kuti mudzafuna kukambitsirana zamkati mwake ndi munthu wina amene amazindikira bwino Baibulo, chifukwa chakuti zinthu zimenezi zimakhudza kwambiri miyoyo ya ife tonse. Aka kadzakukhozetsani kuwona mmene. Baibulo lenilenilo limayankhira mafunso anu. Mboni za Yehova zidzakondwa kusonyeza, kwaulere, mmene makambitsirano oterowo angakhalire opindulitsa.
—AFALITSI