Mutu wa Buku Lino/Tsamba la Ofalitsa
Mbiri Yabwino Yokusangalatsani
Kodi pali mbiri yabwino iri yonse kaamba ka anthu lero lino? Inde, iripo! Ndiyo “mbiri yabwino ya chisangalalo chachikulu chimene anthu onse adzakhala nacho”—pa dziko lonse lapansi. Imakhudza moyo wa ali yense wa ife tsopano, ndipo imasimba za m’tsogolo mwaulemerero m’mene inu ndi okondedwa anu mungakhalemo. Ndiyo mbiri yabwino yokusangalatsani.
—Afalitsi