Za M’katimu
TSAMBA MUTU
5 1 Kodi Mbiri Yabwino Ingapezeke Kuti Lero Lino?
10 2 Kupanga Bukhu la Mbiri Yabwino
29 4 Chitsogozo Chopindulitsa ku Chimwemwe Cheni-cheni
39 5 M’mene Mbiri Yabwino Inasungidwira
48 6 Magwero a Mbiri Yabwino—“Mulungu”
58 7 Kulinganizira Anthu Malo Okhala Achimwemwe
66 8 Mlengi Aika Okhala pa “Chombo cha m’Mlengalenga Dziko Lapansi”
75 9 Uchimo Uchotsera Anthu Chimwemwe
85 10 Chimene Chimatichitikira Pamene Tifa
95 11 Mulungu Samazunza Miyoyo
106 12 Kodi N’chifukwa Ninji Mulungu Walola Kupanda Chimwemwe?
116 13 Chimasuko ku Imfa Kumka ku Moyo
124 14 Kulambira Mulungu Wamoyo
133 15 Kukhulupirira Malaulo Kungatsogolere ku Kupanda Chimwemwe
141 16 Kupanga Dziko Limodzi Pansi pa Ufumu wa Mulungu
151 17 Paradaiso wa Chisangalalo kaamba ka Anthu Onse
160 18 Mabanja Achimwemwe m’Chifuno cha Mulungu
166 19 Ana—“Cholandira cha kwa Yehova”
174 20 Njira ya Moyo Imene Imatsogolera ku Chimwemwe
183 21 Mulungu Apanga “Zinthu Zonse Kukhala Zatsopano”
TAMVERANI: Mau a Baibulo ogwidwa m’bukhu lino ngochokera mu Revised Untion Nyanja Version. Chizindikiro’cho NW chimasonyeza Baibulo lolembedwa’nso la 1971 la chinenero chamakono la New World Translation of the Holy Scriptures.
Ponena za madeti, chidule’cho B.C.E chimatanthauza “Nyengo Ino Isanakhale,” ndipo C.E chimatanthauza “A Nyengo Ino.”