Mutu wa Buku Lino/Tsamba la Ofalitsa
Munthu Wamkulu Woposa Onse Amene Anakhalako
Losindikizidwa mu 2006
Buku lino lafalitsidwa monga mbali ya ntchito yophunzitsa anthu Baibulo yomwe ikuchitika padziko lonse. Ntchitoyi imayendetsedwa ndi zopereka zaufulu.
Malemba m’buku lino akuchokera m’Baibulo la Buku Lopatulika Ndilo Mau a Mulungu, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina. Komabe, Chichewacho tachilemba m’kalembedwe katsopano. Pamene tasonyeza NW, ndiye kuti lembalo lachokera m’Baibulo la New World Translation of the Holy Scriptures—With References
Magwero a Zithunzithunzi
Mapu kutsogolo kwa Mutu 1: ochokera pamapu ojambulidwanso ndi Pictorial Archive (Near Eastern History) Est. and Survey of Israel