Zamkati
5 Kubadwa kwa Yesu—Kuti Ndipo Liti?
8 Kuthaŵa Wolamulira Wankhalwe
9 Moyo Wabanja Woyambirira wa Yesu
13 Kuphunzira Kuchokera Kuziyeso za Yesu
15 Chozizwitsa Choyamba cha Yesu
16 Changu cha Kulambira Yehova
19 Kuphunzitsa Mkazi wa ku Samariya
20 Chozizwitsa Chachiŵiri Ali m’Kana
21 M’Sunagoge wa Tauni ya Kwawo kwa Yesu
23 Zozizwitsa Zowonjezereka m’Kapernao
24 Chifukwa Chake Yesu Anadza Kudziko Lapansi
28 Afunsidwa za Kusala Chakudya
29 Kuchita Ntchito Zabwino pa Sabata
32 Kodi Chololeka Nchiyani pa Sabata?
33 Kukwaniritsa Ulosi wa Yesaya
35 Ulaliki Wotchuka Woposa Wonse Umene Unaperekedwa
36 Chikhulupiliro Chachikulu cha Kazembe Wankhondo
37 Yesu Achotsa Chisoni cha Mkazi Wamasiye
38 Kodi Yohane Anasoŵa Chikhulupiliro?
44 Kutontholetsa Namondwe Wochititsa Mantha
45 Wophunzira Wosayembekezeredwa
47 Misozi Isanduka Chikondwerero Chachikulu
48 Kuchoka Panyumba ya Yairo ndi Kukachezanso ku Nazarete
49 Ulendo Wina Wokalalikira ku Galileya
50 Kukonzekera Kuyang’anizana ndi Chizunzo
51 Kupha Mwambanda pa Phwando la Tsiku Lakubadwa
52 Yesu Adyetsa Zikwi Zambiri Mozizwitsa
53 Wolamulira Woposa Waumunthu Wokhumbidwayo
55 Ophunzira Ambiri Aleka Kutsatira Yesu
56 Kodi Chimaipitsa Munthu Nchiyani?
57 Kuchitira Chifundo Okanthidwa
58 Mitanda ya Mikate ndi Chotupitsa
59 Kodi Yesu Kwenikweni Ndani?
60 Kuwoneratu Ulemelero wa Ufumu wa Kristu
61 Mnyamata Wogwidwa ndi Chiŵanda Achiritsidwa
63 Uphungu Wowonjezereka wa Kuwongolera
65 Ulendo Wakachetechete wa ku Yerusalemu
68 Kuphunzitsa Kowonjezereka Patsiku la Chisanu ndi Chiŵiri
70 Kuchiritsa Munthu Wosawona Chibadwire
71 Afarisi Akana Dala Kukhulupirira
74 Uphungu kwa Marita, ndi Chilangizo pa Pemphero
76 Kudyera Limodzi ndi Mfarisi
79 Mtundu Wotayika, Koma Osati Wonse
80 Mtundu Wotayika, Koma Osati Wonse
81 Kuyesayesa Kowonjezereka kwa Kupha Yesu
82 Yesu Apitanso ku Yerusalemu
84 Thayo la Kukhala Wophunzira
87 Linganizani Mtsogolo Mwanzeru Yogwira Ntchito
89 Ulendo Wokasonyeza Chifundo m’Yudeyaa
90 Chiyembekezo cha Chiukiriro
92 Akhate Khumi Achiritsidwa Mkati mwa Ulendo Wotsirizira wa Yesu Womka ku Yerusalemu
93 Pamene Mwana wa Munthu Avumbulutsidwa
94 Kufunika kwa Pemphero ndi kwa Kudzichepetsa
95 Maphunziro Onena za Chisudzulo ndi Kukonda Ana
96 Yesu ndi Woweruza Wachichepere Wachuma
97 Ogwira Ntchito m’Munda Wampesa
98 Ophunzira Akangana Pamene Imfa ya Yesu Iyandikira
101 Ku Betaniya, m’Nyumba ya Simoni
102 Kuloŵa m’Yerusalemu Kwachipambano kwa Kristu
103 Kufika Pakachisi Kachiŵirinso
104 Liwu la Mulungu Limveka Kachitatu
105 Kuyamba kwa Tsiku Lofunika Koposa
106 Avumbulidwa ndi Mafanizo a Munda Wampesa
107 Fanizo la Phwando Laukwati
110 Uminisitala wa Pakachisi Umalizidwa
111 Chizindikiro cha Masiku Otsiriza
112 Paskha Womalizira wa Yesu Wayandikira
113 Kudzichepetsa pa Paskha Womalizira
116 Kukonzekeretsa Atumwi Kaamba ka Kuchoka Kwake
119 Atengeredwa kwa Anasi, Ndiyeno kwa Kayafa
120 Kukanidwa m’Bwalo Lamilandu
121 Pamaso pa Sanhedrin, Ndiyeno kwa Pilato
122 Kuchokera kwa Pilato Kumka kwa Herode ndi Kubwereranso
126 “Zowonadi Uyu Anali Mwana wa Mulungu”
127 Kuikidwa m’Manda Lachisanu—Manda Apululu pa Lamlungu
131 Kuwonekera Komaliza, ndi Pentekoste wa 33 C.E.
132 Kudzanja Lamanja la Mulungu
133 Yesu Achita Zonse Zimene Mulungu Afuna