Zamkatimu
Mutu Tsamba
GAWO 1-Mulungu Angakuthandizeni Kukonzekera Tsiku Lake Lalikulu.
5 1. Uthenga Umene Yehova Anapereka Kalelo Ndi Wothandizanso Masiku Ano
14 2. Aneneri Amene Uthenga Wawo Ungatithandize
29 3. Mfundo Yaikulu mu Uthenga wa Aneneri 12 Inali Yokhudza Tsiku la Yehova
GAWO 2-Dziwani Yehova Ndipo Mutumikireni
43 4. Yehova Ndi Mulungu Amene Amalosera Zam’tsogolo N’kuzikwaniritsa
56 5. ‘Funafunani Yehova’ Pomulambira M’njira Imene Amavomereza
70 6. Kuchita Zinthu ‘Mwachilungamo’ N’kofunika Kwambiri Kuti Timudziwe Mulungu
83 7. Tumikirani Yehova Mogwirizana ndi Mfundo Zake Zabwino Kwambiri
GAWO 3-Yesetsani Kuchita Zinthu Zosangalatsa Mulungu
97 8. “Kodi Yehova Akufuna Chiyani Kwa Iwe?”
111 9. Muzichitira Ena Zimene Mulungu Amafuna
124 10. Yesetsani Kuti Banja Lanu Lizikondweretsa Mulungu
GAWO 4-Yembekezerani Tsiku la Yehova Mosangalala
139 11. Kodi Mukufuna Kuti Anthu Adzapeze Moyo Wosatha Ngati Mmene Yehova Akufunira?
152 12. ‘Muziyembekezerabe’ Tsiku la Yehova
165 13. ‘Anthu Inu, Lengezani Uthengawu Pakati pa Mitundu Ina’