Zamkatimu
7 1 Kodi Ndingatani Kuti Ndizilankhula Momasuka Ndi Makolo Anga?
14 2 N’chifukwa Chiyani Ndimangokhalira Kukangana Ndi Makolo Anga?
21 3 Kodi Ndingatani Kuti Makolo Anga Azindilolako Kuchita Zinthu Zina?
28 4 N’chifukwa Chiyani Banja la Makolo Anga Linatha?
34 5 Kodi Ndingatani Ngati Makolo Anga Akwatiranso?
40 6 Kodi Ndingatani Kuti Ndizigwirizana Ndi Abale Anga?
49 7 Kodi Ndine Wokonzeka Kusamuka N’kumakakhala Ndekha?
57 8 Kodi Ndingapeze Bwanji Anzanga Abwino?
64 9 Kodi Ndingatani Kuti Ndisamakopeke Ndi Zochita za Anzanga?
71 10 N’chifukwa Chiyani Ndiyenera Kusamalira Thanzi Langa?
85 12 Kodi Ndingatani Kuti Ndisamadziderere?
91 13 Kodi Ndingatani Kuti Ndisamangokhala Wokhumudwa?
105 15 Kodi N’kulakwa Kufuna Kuchitako Zinthu Zina Pandekha?
111 16 N’chiyani Chingandithandize Kupirira Ngati Mayi Kapena Bambo Anga Anamwalira?
121 17 N’chifukwa Chiyani Ndimaopa Kuuza Anzanga Akusukulu Zimene Ndimakhulupirira?
128 18 Kodi Ndingatani Ngati Ndimapanikizika Kwambiri Kusukulu?
134 19 Bwanji Ndingosiya Sukulu?
142 20 Kodi Ndingatani Kuti Ndizigwirizana Ndi Aphunzitsi Anga?
150 21 Kodi Ndingatani Kuti Ndizigwiritsa Ntchito Nthawi Yanga Mwanzeru?
156 22 Kodi Nditsatire Chikhalidwe Chiti?
172 24 Kodi Kugonana Tili Pachibwenzi Kungachititse Kuti Tizikondana Kwambiri?
178 25 Kodi Ndingatani Kuti Ndisiye Chizolowezi Choseweretsa Maliseche?
183 26 Kodi Kugonana Pongofuna Kuthandizana Kuli Ndi Vuto?
188 27 N’chifukwa Chiyani Anyamata Samandifunsira?
195 28 N’chifukwa Chiyani Atsikana Samandifuna?
203 29 Kodi Ndingadziwe Bwanji Ngati Chilidi Chikondi Chenicheni?
212 30 Kodi Ndife Okonzeka Kulowa M’banja?
221 31 Kodi Ndingatani Ngati Chibwenzi Chatha?
228 32 Kodi Ndingadziteteze Bwanji Kwa Anthu Ogwiririra Anzawo?
237 33 Kodi Mumadziwa Zotani pa Nkhani ya Fodya?
246 34 Kodi Kumwa Mowa Wambiri Kuli Ndi Vuto Lanji?
252 35 Kodi Ndingatani Kuti Ndisiye Kugwiritsa Ntchito Mankhwala Osokoneza Bongo?
259 36 Kodi Ndimagwiritsa Ntchito Zipangizo Zamakono Mopitirira Muyezo?
265 37 N’chifukwa Chiyani Makolo Anga Samandilola Kuti Ndizisangalalako Nthawi Zina?
273 38 Kodi Ndingatani Kuti Kulambira Mulungu Kuzindisangalatsa?
282 39 Kodi Ndingatani Kuti Ndikwaniritse Zolinga Zanga?
289 Zakumapeto: Mafunso Amene Makolo Amadzifunsa