Mutu wa Buku Lino/Tsamba la Ofalitsa
Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo
Bukuli ndi la ․․․․․
Bukuli sitigulitsa. Timalipereka ngati njira imodzi yophunzitsa anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka ndalama, pitani pa webusaiti ya www.pr418.com/ny
Malemba onse m’bukuli akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
Kasindikizidwa mu August 2016
Chichewa (ia-CN)
© 2013
WATCH TOWER BIBLE AND TRACT SOCIETY OF PENNSYLVANIA