Zimene Zili M’bukuli
MUTU
Mawu Oyamba Gawo 1—Ntchito Yolenga
1 Mulungu Analenga Kumwamba ndi Dziko Lapansi
2 Mulungu Analenga Mwamuna ndi Mkazi Oyamba
Mawu Oyamba Gawo 2—Kuyambira Nthawi ya Adamu Mpaka Nthawi ya Chigumula
3 Adamu ndi Hava Sanamvere Mulungu
4 Kaini Anakwiya Mpaka Anapha M’bale Wake
Mawu Oyamba Gawo 3—Kuyambira Nthawi ya Chigumula Mpaka Nthawi ya Yakobo
8 Abulahamu ndi Sara Anamvera Mulungu
9 Anakhala ndi Mwana Atakalamba
11 Abulahamu Anasonyeza Kuti Anali Wokhulupirika
12 Yakobo Analandira Madalitso
13 Yakobo ndi Esau Anagwirizananso
Mawu Oyamba Gawo 4—Kuyambira Nthawi ya Yosefe Mpaka pa Nyanja Yofiira
14 Kapolo Amene Ankamvera Mulungu
17 Mose Anasankha Kuti Azilambira Yehova
22 Zodabwitsa Zimene Zinachitika pa Nyanja Yofiira
Mawu Oyamba Gawo 5—Aisiraeli Ali M’chipululu
23 Analonjeza Kuti Azimvera Yehova
24 Aisiraeli Sanachite Zimene Analonjeza
26 Anthu 12 Anapita Kukafufuza Dziko la Kanani
27 Aisiraeli Ena Anaukira Yehova
30 Rahabi Anabisa Aisiraeli Okafufuza Dziko
31 Yoswa ndi Anthu a ku Gibiyoni
32 Mtsogoleri Watsopano Komanso Azimayi Awiri Olimba Mtima
34 Gidiyoni Anagonjetsa Amidiyani
35 Hana Anapempha Mwana Wamwamuna
37 Yehova Analankhula ndi Samueli
38 Yehova Anapatsa Mphamvu Samisoni
Mawu Oyamba Gawo 7—Davide ndi Sauli
42 Yonatani Anali Wolimba Mtima Komanso Wokhulupirika
Mawu Oyamba Gawo 8—Kuyambira Nthawi ya Solomo Mpaka Nthawi ya Eliya
46 Zimene Zinachitika Paphiri la Karimeli
48 Mwana wa Mayi Wamasiye Anaukitsidwa
49 Mfumukazi Yoipa Inalangidwa
50 Yehova Anathandiza Mfumu Yehosafati
Mawu Oyamba Gawo 9—Kuyambira Nthawi ya Elisa Mpaka Nthawi ya Yosiya
51 Kamtsikana Kanathandiza Mkulu wa Asilikali
52 Gulu Lamphamvu la Asilikali a Yehova
53 Yehoyada Anali Wolimba Mtima
54 Yehova Analezera Mtima Yona
55 Mngelo wa Yehova Anateteza Hezekiya
56 Yosiya Ankakonda Chilamulo cha Mulungu
Mawu Oyamba Gawo 10—Kuyambira Nthawi ya Yeremiya Mpaka Nthawi ya Nehemiya
57 Yehova Anauza Yeremiya Kuti Azilalikira
58 Mzinda wa Yerusalemu Unawonongedwa
59 Anyamata 4 Amene Anamvera Yehova
60 Ufumu Umene Udzalamulire Mpaka Kalekale
62 Ufumu Wofanana ndi Mtengo Waukulu
64 Danieli Anaponyedwa M’dzenje la Mikango
65 Esitere Anapulumutsa Anthu a Mtundu Wake
66 Ezara Ankaphunzitsa Chilamulo cha Mulungu
67 Mpanda wa Yerusalemu Unamangidwanso
Mawu Oyamba Gawo 11—Yohane M’batizi ndi Yesu
68 Elizabeti Anakhala ndi Mwana
69 Gabirieli Analankhula ndi Mariya
70 Angelo Analengeza za Kubadwa kwa Yesu
72 Zimene Yesu Anachita Ali Wamng’ono
Mawu Oyamba Gawo 12—Utumiki wa Yesu Padzikoli
77 Yesu Anakumana ndi Mayi Pachitsime
78 Yesu Ankalalikira Uthenga wa Ufumu
79 Yesu Anachita Zozizwitsa Zambiri
82 Yesu Anaphunzitsa Otsatira Ake Kupemphera
83 Yesu Anadyetsa Anthu Ambiri
85 Yesu Anachiritsa Munthu pa Tsiku la Sabata
Mawu Oyamba Gawo 13—Chakumapeto kwa Utumiki wa Yesu
87 Chakudya Chamadzulo Chomaliza
Mawu Oyamba Gawo 14—Chikhristu Chinayamba Kufalikira
94 Ophunzira a Yesu Analandira Mzimu Woyera
97 Koneliyo Analandira Mzimu Woyera
98 Anthu a Mitundu Ina Anamva Uthenga Wabwino
99 Woyang’anira Ndende Anaphunzira Mawu a Yehova
101 Paulo Anatumizidwa ku Roma