Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • lfb tsamba 218-219
  • Mawu Oyamba Gawo 14

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Mawu Oyamba Gawo 14
  • Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
  • Nkhani Yofanana
  • Zimene Yohane Anaona M’masomphenya
    Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
  • Tsanzirani Yesu mwa Kulalikira Molimba Mtima
    Nsanja ya Olonda—2009
  • Kodi Ufumu wa Mulungu N’chiyani?
    Kodi Mulungu Amafunanji kwa Ife?
  • Kodi Yesu Anaphunzitsa Chiyani za Ufumu wa Mulungu?
    Nsanja ya Olonda—2010
Onani Zambiri
Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
lfb tsamba 218-219
Mtumwi Paulo ndi Timoteyo ali mungalawa

Mawu Oyamba Gawo 14

Akhristu oyambirira analalikira uthenga wabwino wa Ufumu m’madera ambiri padzikoli. Yesu ankawatsogolera kuti adziwe kokalalikira ndiponso anawathandiza kulalikira m’zilankhulo zina. Yehova anawathandizanso kuti akhale olimba mtima komanso anawapatsa mphamvu kuti azipirira akamazunzidwa.

Yesu anaonetsa mtumwi Yohane masomphenya a ulemerero wa Yehova. M’masomphenya ena anamuonetsa Ufumu wakumwamba ukugonjetsa Satana n’kumuchititsa kuti asamasocheretsenso anthu. Yohane anaona Yesu akulamulira limodzi ndi anthu 144,000. Anaonanso dziko lonse lili Paradaiso komanso anthu onse akulambira Yehova mogwirizana.

ZIMENE TIPHUNZIRE M’CHIGAWOCHI

  • Tikamagwira ntchito imene tinapatsidwa timalemekeza Yehova

  • Tiyenera kudzipereka kwa Yehova n’kumachita zinthu zosonyeza kuti tikufuna kudzalamuliridwa ndi Ufumu wake

  • Tiziyesetsa kuti Yehova akhale mnzathu wapamtima

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena